-
Deuteronomo 32:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Anamudyetsa uchi wochokera mʼthanthwe,
Ndi mafuta ochokera mʼmwala wa nsangalabwi.
14 Anamudyetsanso mafuta a mkaka wa ngʼombe ndi mkaka wa nkhosa,
Pamodzi ndi nkhosa zabwino kwambiri,*
Komanso nkhosa zamphongo za ku Basana ndi mbuzi zamphongo,
Pamodzi ndi tirigu wabwino koposa.*+
Ndipo munamwa vinyo wochokera mʼmagazi a mphesa.*
-