Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezera kuti: “Ndaona mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuvutikira, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Ndikudziwa bwino ululu umene akumva.+
7 Yehova anawonjezera kuti: “Ndaona mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuvutikira, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Ndikudziwa bwino ululu umene akumva.+