-
Yesaya 6:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Pamwamba pake panali aserafi. Mserafi aliyense anali ndi mapiko 6. Aliyense anaphimba nkhope yake ndi mapiko awiri, anaphimba mapazi ake ndi mapiko awiri ndipo mapiko ena awiriwo ankaulukira.
3 Aliyense ankauza mnzake kuti:
“Woyera, woyera, woyera ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+
Dziko lonse lapansi ladzaza ndi ulemerero wake.”
-