2 Samueli 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Yehova ndi wamoyo! Litamandike Thanthwe langa!+ Mulungu wanga, yemwe ndi thanthwe limene limandipulumutsa, alemekezeke.+ Salimo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+
47 Yehova ndi wamoyo! Litamandike Thanthwe langa!+ Mulungu wanga, yemwe ndi thanthwe limene limandipulumutsa, alemekezeke.+
2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+