Deuteronomo 28:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anthu adzachita mantha akadzaona zimene zakuchitikirani ndipo mudzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu kumene Yehova akukuthamangitsirani.+
37 Anthu adzachita mantha akadzaona zimene zakuchitikirani ndipo mudzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu kumene Yehova akukuthamangitsirani.+