Deuteronomo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Panadutsa zaka 38 kuti tiyende kuchokera ku Kadesi-barinea nʼkuwoloka chigwa cha Zeredi,* mpaka mʼbadwo wonse wa amuna opita kunkhondo utatha pakati pathu, mogwirizana ndi zimene Yehova analumbira kwa iwo.+
14 Panadutsa zaka 38 kuti tiyende kuchokera ku Kadesi-barinea nʼkuwoloka chigwa cha Zeredi,* mpaka mʼbadwo wonse wa amuna opita kunkhondo utatha pakati pathu, mogwirizana ndi zimene Yehova analumbira kwa iwo.+