Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu. 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu.
9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+