Salimo 16:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzatamanda Yehova amene wandipatsa malangizo.+ Ngakhale usiku maganizo amkati mwa mtima wanga* amandiuza zoyenera kuchita.+ 8 Ndimaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+ Chifukwa iye ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.*+ Miyambo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Palibe munthu amene angakhale wotetezeka chifukwa chochita zoipa,+Koma anthu olungama sadzazulidwa. 2 Petulo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho abale, chitani chilichonse chotheka kuti mukhalebe okhulupirika, nʼcholinga choti mupitirizebe kukhala pakati pa anthu amene Mulungu wawaitana+ ndi kuwasankha. Mukapitiriza kuchita zimenezi, simudzalephera ngakhale pangʼono.+
7 Ndidzatamanda Yehova amene wandipatsa malangizo.+ Ngakhale usiku maganizo amkati mwa mtima wanga* amandiuza zoyenera kuchita.+ 8 Ndimaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+ Chifukwa iye ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.*+
3 Palibe munthu amene angakhale wotetezeka chifukwa chochita zoipa,+Koma anthu olungama sadzazulidwa.
10 Choncho abale, chitani chilichonse chotheka kuti mukhalebe okhulupirika, nʼcholinga choti mupitirizebe kukhala pakati pa anthu amene Mulungu wawaitana+ ndi kuwasankha. Mukapitiriza kuchita zimenezi, simudzalephera ngakhale pangʼono.+