Levitiko 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Choncho ndidzakumbukira pangano limene ndinachita ndi Yakobo,+ Isaki+ komanso Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo. Luka 1:54, 55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Iye wathandiza mtumiki wake Isiraeli pokumbukira lonjezo lake lakuti adzasonyeza chifundo+ 55 kwamuyaya, mogwirizana ndi zimene anauza makolo athu akale, Abulahamu ndi mbadwa* zake.”+
42 Choncho ndidzakumbukira pangano limene ndinachita ndi Yakobo,+ Isaki+ komanso Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.
54 Iye wathandiza mtumiki wake Isiraeli pokumbukira lonjezo lake lakuti adzasonyeza chifundo+ 55 kwamuyaya, mogwirizana ndi zimene anauza makolo athu akale, Abulahamu ndi mbadwa* zake.”+