Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wosangalala ndi munthu amene inu mwamusankha nʼkumubweretsa pafupi ndi inu,Kuti akhale mʼmabwalo anu.+ Tidzakhutira ndi zinthu zabwino zamʼnyumba yanu,+Kachisi wanu woyera.*+
4 Wosangalala ndi munthu amene inu mwamusankha nʼkumubweretsa pafupi ndi inu,Kuti akhale mʼmabwalo anu.+ Tidzakhutira ndi zinthu zabwino zamʼnyumba yanu,+Kachisi wanu woyera.*+