Ekisodo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atatero Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo muona mmene Yehova akupulumutsireni lero.+ Chifukwa Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso mpaka kalekale.+ Ekisodo 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Madzi amene anabwererawo anamiza magaleta ankhondo, asilikali apamahatchi ndi gulu lonse lankhondo la Farao, amene analondola Aisiraeli mʼnyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+
13 Atatero Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo muona mmene Yehova akupulumutsireni lero.+ Chifukwa Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso mpaka kalekale.+
28 Madzi amene anabwererawo anamiza magaleta ankhondo, asilikali apamahatchi ndi gulu lonse lankhondo la Farao, amene analondola Aisiraeli mʼnyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+