Numeri 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Mose ndi Aroni anasonkhanitsa mpingo wonse pamodzi patsogolo pa thanthwelo, ndipo Mose anawauza kuti: “Tsopano tamverani anthu opanduka inu! Kodi tikutulutsireni madzi mʼthanthweli?”+
10 Kenako Mose ndi Aroni anasonkhanitsa mpingo wonse pamodzi patsogolo pa thanthwelo, ndipo Mose anawauza kuti: “Tsopano tamverani anthu opanduka inu! Kodi tikutulutsireni madzi mʼthanthweli?”+