Ekisodo 23:32, 33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Musamachite pangano ndi iwo kapena milungu yawo.+ 33 Asamakhale mʼdziko lanu kuti asakuchititseni kuti mundichimwire. Mukadzatumikira milungu yawo, udzakhala msampha ndithu kwa inu.”+
32 Musamachite pangano ndi iwo kapena milungu yawo.+ 33 Asamakhale mʼdziko lanu kuti asakuchititseni kuti mundichimwire. Mukadzatumikira milungu yawo, udzakhala msampha ndithu kwa inu.”+