18 Yehova akawapatsa woweruza,+ Yehova ankakhala ndi woweruzayo, ndipo ankawapulumutsa mʼmanja mwa adani awo pa nthawi yonse ya woweruzayo. Yehova ankawamvera chisoni+ akamva kulira kwawo chifukwa cha anthu omwe ankawapondereza+ komanso kuwachitira nkhanza.