1 Mbiri 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nenani kuti: ‘Tipulumutseni, inu Mulungu wachipulumutso chathu,+Tisonkhanitseni ndi kutipulumutsa kwa anthu a mitundu ina,Kuti titamande dzina lanu loyera,+Ndiponso kuti tikutamandeni mosangalala.+
35 Nenani kuti: ‘Tipulumutseni, inu Mulungu wachipulumutso chathu,+Tisonkhanitseni ndi kutipulumutsa kwa anthu a mitundu ina,Kuti titamande dzina lanu loyera,+Ndiponso kuti tikutamandeni mosangalala.+