21 (Chifukwa pali amuna ena amene akhala ansembe popanda lumbiro, koma ameneyu wakhala wansembe pochita kumulumbirira. Lumbiro limeneli ndi la amene ananena za wansembeyo kuti: “Yehova walumbira kuti, ‘Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,’ ndipo sadzasintha maganizo.”)+