Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani? Miyambo 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Sudzaopa zoopsa zilizonse zadzidzidzi,+Kapena mphepo yamkuntho imene ikubwera pa oipa.+
27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani?