Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muzimudalira nthawi zonse, anthu inu. Mukhuthulireni zonse zamumtima mwanu.+ Mulungu ndi malo athu othawirako.+ (Selah) Yesaya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+
8 Muzimudalira nthawi zonse, anthu inu. Mukhuthulireni zonse zamumtima mwanu.+ Mulungu ndi malo athu othawirako.+ (Selah)
3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+