-
Yeremiya 10:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Miyambo ya anthu amenewa ndi yopanda pake.
-
-
Yeremiya 10:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Onse ndi opanda nzeru ndiponso opusa.+
Malangizo ochokera pamtengo amalimbikitsa anthu kuchita zachabechabe.+
9 Siliva amene anamusula kukhala mapalemapale amachokera ku Tarisi+ ndipo golide amachokera ku Ufazi.
Zonsezi zimakonzedwa mwaluso ndipo ndi ntchito ya manja a mmisiri wa zitsulo.
Amawaveka zovala zaulusi wabuluu ndi ubweya wa nkhosa wapepo.
Mafano onsewo amapangidwa ndi amisiri aluso.
-
-
1 Akorinto 10:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kodi mfundo yake ndi yotani? Kodi zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano kapena mafano enieniwo ndi kanthu?
-