Chivumbulutso 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu kumwamba amene ankamveka ngati mawu ofuula a khamu lalikulu akuti: “Tamandani Ya!*+ Mulungu wathu amapulumutsa anthu ndipo ali ndi mphamvu zazikulu komanso ulemerero,
19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu kumwamba amene ankamveka ngati mawu ofuula a khamu lalikulu akuti: “Tamandani Ya!*+ Mulungu wathu amapulumutsa anthu ndipo ali ndi mphamvu zazikulu komanso ulemerero,