Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani?
27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani?