6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,
Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.+
7 Atakugwira dzanja, unaphwanyika,
Ndipo unachititsa kuti athyole phewa lawo.
Atakutsamira ngati ndodo yoyendera, unathyoka,
Ndipo unachititsa kuti miyendo yawo injenjemere.”+