Ekisodo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+ Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+ Salimo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+ Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+
2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+
2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+