Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akundiyamikira kuti ikhale nsembe imene akupereka kwa ine akundilemekeza.+Ndipo munthu amene akupitiriza kuchita zabwino,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Hoseya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo. Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+
23 Amene akundiyamikira kuti ikhale nsembe imene akupereka kwa ine akundilemekeza.+Ndipo munthu amene akupitiriza kuchita zabwino,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo.
15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+