Salimo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mʼmawa mudzamva mawu anga,+Mʼmawa ndidzafotokoza nkhawa zanga kwa inu+ ndipo ndidzadikira yankho lanu. Salimo 88:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndimafuulirabe kwa inu Yehova kuti mundithandize,+Mʼmawa uliwonse pemphero langa limafika kwa inu.+ Maliko 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mʼmawa kwambiri kudakali mdima, Yesu anadzuka nʼkutuluka panja ndipo anapita kumalo kopanda anthu. Kumeneko anayamba kupemphera.+
3 Inu Yehova, mʼmawa mudzamva mawu anga,+Mʼmawa ndidzafotokoza nkhawa zanga kwa inu+ ndipo ndidzadikira yankho lanu.
13 Koma ine ndimafuulirabe kwa inu Yehova kuti mundithandize,+Mʼmawa uliwonse pemphero langa limafika kwa inu.+
35 Mʼmawa kwambiri kudakali mdima, Yesu anadzuka nʼkutuluka panja ndipo anapita kumalo kopanda anthu. Kumeneko anayamba kupemphera.+