Salimo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuopa Yehova+ nʼkoyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya. Zigamulo za Yehova nʼzolondola, ndipo pa mbali iliyonse ndi zolungama.+ Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni* pogwiritsa ntchito choonadi.+ Mawu anu ndi choonadi.+
9 Kuopa Yehova+ nʼkoyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya. Zigamulo za Yehova nʼzolondola, ndipo pa mbali iliyonse ndi zolungama.+