Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakonda kwambiri chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kuganizira mozama* chilamulocho masana ndi usiku.+ Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimasangalala* kuchita zimene mumafuna, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga ndimasangalala kwambiri ndi malamulo a Mulungu,+
2 Koma amakonda kwambiri chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kuganizira mozama* chilamulocho masana ndi usiku.+
8 Ndimasangalala* kuchita zimene mumafuna, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+