2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhalapobe mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 1 Mafumu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mfumuyo inapanganso mpando wachifumu waukulu waminyanga ya njovu+ nʼkuukuta ndi golide woyenga bwino.+ 1 Mbiri 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho, Solomo anakhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu mʼmalo mwa Davide bambo ake ndipo zinthu zinkamuyendera bwino. Aisiraeli onse ankamumvera.
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhalapobe mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
18 Mfumuyo inapanganso mpando wachifumu waukulu waminyanga ya njovu+ nʼkuukuta ndi golide woyenga bwino.+
23 Choncho, Solomo anakhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu mʼmalo mwa Davide bambo ake ndipo zinthu zinkamuyendera bwino. Aisiraeli onse ankamumvera.