Genesis 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu+ amʼbadwo wachitatu. Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamawondo a Yosefe.*
23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu+ amʼbadwo wachitatu. Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamawondo a Yosefe.*