Ekisodo 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mʼdziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku a moyo wanu.* Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndi mphoto yochokera kwa Mulungu.+
26 Mʼdziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku a moyo wanu.*
3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndi mphoto yochokera kwa Mulungu.+