Salimo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+ Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima nʼkutipatsa ulemerero. Yehova sadzalephera kupereka chinthu chilichonse chabwinoKwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+
2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+
11 Chifukwa Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima nʼkutipatsa ulemerero. Yehova sadzalephera kupereka chinthu chilichonse chabwinoKwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+