Salimo 119:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Inu ndinu wabwino+ ndipo ntchito zanu ndi zabwino. Ndiphunzitseni malamulo anu.+ Mateyu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukundifunsa zokhudza zinthu zabwino? Pali mmodzi yekha amene ndi wabwino.+ Choncho ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+
17 Iye anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukundifunsa zokhudza zinthu zabwino? Pali mmodzi yekha amene ndi wabwino.+ Choncho ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+