Deuteronomo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova nʼkumamutumikira komanso kuti lizidalitsa anthu mʼdzina lake+ ngati mmene akuchitira mpaka lero.
8 Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova nʼkumamutumikira komanso kuti lizidalitsa anthu mʼdzina lake+ ngati mmene akuchitira mpaka lero.