29 Ndiyeno pakati pa usiku, Yehova anapha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo.+ Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene anali pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa mkaidi amene anali mʼndende, ndiponso mwana aliyense woyamba kubadwa wa nyama.+