Yobu 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu mudzaitana ndipo ine ndidzakuyankhani.+ Mudzalakalaka ntchito ya manja anu. Salimo 71:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale nditakalamba nʼkumera imvi, inu Mulungu musandisiye.+ Ndiloleni kuti ndiuze mʼbadwo wotsatira za mphamvu zanu*Komanso za nyonga zanu kwa onse obwera mʼtsogolo.+
18 Ngakhale nditakalamba nʼkumera imvi, inu Mulungu musandisiye.+ Ndiloleni kuti ndiuze mʼbadwo wotsatira za mphamvu zanu*Komanso za nyonga zanu kwa onse obwera mʼtsogolo.+