2 Mbiri 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya, anapita kwa Mfumu Yehosafati ndipo anamufunsa kuti: “Kodi muyenera kuthandiza anthu oipa,+ ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani. 2 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamangidwe mʼgoli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali mgwirizano wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+
2 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya, anapita kwa Mfumu Yehosafati ndipo anamufunsa kuti: “Kodi muyenera kuthandiza anthu oipa,+ ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani.
14 Musamangidwe mʼgoli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali mgwirizano wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+