2 Samueli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anagonjetsa Hadadezeri, mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kumtsinje wa Firate+ kukabwezeretsa ulamuliro wake. Salimo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tandipempha, ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kuti ikhale cholowa chako,Ndiponso dziko lonse lapansi kuti likhale lako.+
3 Davide anagonjetsa Hadadezeri, mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kumtsinje wa Firate+ kukabwezeretsa ulamuliro wake.
8 Tandipempha, ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kuti ikhale cholowa chako,Ndiponso dziko lonse lapansi kuti likhale lako.+