Miyambo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa lamulolo ndi nyale,+Ndipo malangizo ndi kuwala,+Komanso kudzudzula kumene kumathandiza munthu kusintha ndi njira yakumoyo.+ Yakobo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali aliyense amene akudwala pakati panu? Aitane akulu+ a mpingo, ndipo iwo amupempherere ndi kumupaka+ mafuta mʼdzina la Yehova.*
23 Chifukwa lamulolo ndi nyale,+Ndipo malangizo ndi kuwala,+Komanso kudzudzula kumene kumathandiza munthu kusintha ndi njira yakumoyo.+
14 Kodi pali aliyense amene akudwala pakati panu? Aitane akulu+ a mpingo, ndipo iwo amupempherere ndi kumupaka+ mafuta mʼdzina la Yehova.*