-
1 Samueli 23:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kodi atsogoleri amumzinda wa Keila adzandipereka mʼmanja mwake? Kodi Sauli abweradi kuno ngati mmene ine mtumiki wanu ndamvera? Yehova Mulungu wa Isiraeli, chonde ndiuzeni ine mtumiki wanu.” Yehova anamuyankha kuti: “Inde abweradi.”
-