Salimo 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimaganiza kuti, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira,Ndipo mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+ Aheberi 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma mboni ina inanena penapake kuti: “Munthu ndi ndani kuti muzimuganizira, kapena mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+
4 Ndimaganiza kuti, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira,Ndipo mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+
6 Koma mboni ina inanena penapake kuti: “Munthu ndi ndani kuti muzimuganizira, kapena mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+