-
2 Mafumu 6:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mtumiki wa munthu wa Mulungu woona atadzuka mʼmawa nʼkutuluka panja, anaona kuti gulu lankhondo lazungulira mzindawo ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo. Nthawi yomweyo mtumikiyo anauza mbuye wake kuti: “Mayo ine mbuyanga! Titani?” 16 Koma iye anati: “Usaope,+ ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi iwowo.”+
-
-
Salimo 27:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,
Pameneponso ndidzadalira Mulungu.
-