Salimo 146:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova akutsegula maso a anthu amene ali ndi vuto losaona.+Yehova akudzutsa anthu amene awerama chifukwa cha mavuto.+Yehova amakonda anthu olungama.
8 Yehova akutsegula maso a anthu amene ali ndi vuto losaona.+Yehova akudzutsa anthu amene awerama chifukwa cha mavuto.+Yehova amakonda anthu olungama.