Machitidwe 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zimene zimakhala mmenemo.+ Chivumbulutso 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye ankanena mofuula kuti: “Opani Mulungu ndi kumupatsa ulemerero chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Choncho lambirani Iye amene anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja+ ndi akasupe amadzi.”
24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zimene zimakhala mmenemo.+
7 Iye ankanena mofuula kuti: “Opani Mulungu ndi kumupatsa ulemerero chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Choncho lambirani Iye amene anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja+ ndi akasupe amadzi.”