Deuteronomo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye amachitira chilungamo ana amasiye ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo+ moti amamupatsa chakudya ndi zovala. Salimo 68:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Bambo wa ana amasiye komanso amene amateteza* akazi amasiye+Ndi Mulungu amene amakhala mʼmalo ake oyera.+
18 Iye amachitira chilungamo ana amasiye ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo+ moti amamupatsa chakudya ndi zovala.
5 Bambo wa ana amasiye komanso amene amateteza* akazi amasiye+Ndi Mulungu amene amakhala mʼmalo ake oyera.+