Yobu 38:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndi ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Komanso akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?” Luka 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ganizirani za akhwangwala: Iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nkhokwe kapena nyumba yosungiramo zinthu, koma Mulungu amawadyetsa.+ Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?+
41 Ndi ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Komanso akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?”
24 Ganizirani za akhwangwala: Iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nkhokwe kapena nyumba yosungiramo zinthu, koma Mulungu amawadyetsa.+ Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?+