Miyambo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo anga ankandiphunzitsa kuti: “Mtima wako ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Uzisunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+ Miyambo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa lamulolo ndi nyale,+Ndipo malangizo ndi kuwala,+Komanso kudzudzula kumene kumathandiza munthu kusintha ndi njira yakumoyo.+ Mateyu 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyale ya thupi ndi diso.+ Choncho ngati diso lako likuyangʼana* pachinthu chimodzi, thupi lako lonse lidzakhala lowala kwambiri.
4 Bambo anga ankandiphunzitsa kuti: “Mtima wako ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Uzisunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+
23 Chifukwa lamulolo ndi nyale,+Ndipo malangizo ndi kuwala,+Komanso kudzudzula kumene kumathandiza munthu kusintha ndi njira yakumoyo.+
22 Nyale ya thupi ndi diso.+ Choncho ngati diso lako likuyangʼana* pachinthu chimodzi, thupi lako lonse lidzakhala lowala kwambiri.