Salimo 63:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma mfumu idzasangalala ndi zimene Mulungu adzaichitire. Munthu aliyense wolumbira mʼdzina la Mulungu adzasangalala kwambiri,*Chifukwa pakamwa pa anthu olankhula zabodza padzatsekedwa.
11 Koma mfumu idzasangalala ndi zimene Mulungu adzaichitire. Munthu aliyense wolumbira mʼdzina la Mulungu adzasangalala kwambiri,*Chifukwa pakamwa pa anthu olankhula zabodza padzatsekedwa.