Yohane 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pambuyo pake, Yesu atadziwa kuti tsopano zonse zachitika, kuti malemba akwaniritsidwe ananena kuti: “Ndikumva ludzu.”+
28 Pambuyo pake, Yesu atadziwa kuti tsopano zonse zachitika, kuti malemba akwaniritsidwe ananena kuti: “Ndikumva ludzu.”+