12 Pa chifukwa chimenechi, ndidzamupatsa gawo pamodzi ndi ambiri,
Ndipo iye adzagawana ndi amphamvu katundu amene alanda kunkhondo,
Chifukwa anapereka moyo wake+
Ndipo anaikidwa mʼgulu la anthu ochimwa.+
Ananyamula tchimo la anthu ambiri+
Ndipo analowererapo kuti athandize anthu ochimwa.+