1 Samueli 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu wanu adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo kuti utetezeke. Koma moyo wa adani anu adzauponya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.*
29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu wanu adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo kuti utetezeke. Koma moyo wa adani anu adzauponya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.*